LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 February tsa. 3
  • Khristu Anavutika Cifukwa ca Ife

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Khristu Anavutika Cifukwa ca Ife
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Nkhani Zofanana
  • Kukwanilitsidwa kwa Maulosi Okhudza Yesu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Kukhala Wokhulupilika kwa Yehova Kumabweletsa Madalitso
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Anthu Angapambane Kokha Ngati Atsogozedwa na Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Zamkatimu
    Galamuka!—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 February tsa. 3

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YESAYA 52-57

Khristu Anavutika Cifukwa ca Ife

“Ananyozedwa ndipo anthu anali kumupewa . . . Tinamuona ngati wosautsidwa wokwapulidwa ndi Mulungu ndiponso wozunzidwa”

53:3-5

  • Anthu anam’nyoza Yesu na kum’namizila kuti anali kunyoza Mulungu. Ena anaganiza kuti Mulungu anali kum’langa

Yesu anali wofunitsitsa kukhala wokhulupilika ngakhale kuti anadziŵa kuti adzavutika

“Koma zinamukomela Yehova kuti mtumiki wake aphwanyidwe. . . . Ndipo ndi dzanja lake, adzakwanilitsa zokonda Yehova”

53:10

  • Sitikukaika kuti cinamuŵaŵa kwambili Yehova kuona Mwana wake akuphedwa. Ngakhale n’conco, iye anakondwela kwambili na kukhulupilika kwa Yesu. Imfa ya Yesu inapeleka yankho pa zimene Satana anakamba zokhudza kukhulupilika kwa atumiki a Mulungu. Ndipo inabweletsa madalitso kwa anthu olapa. Conco, inathandiza kuti “cifunilo ca Mulungu” cikwanilitsike.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani