CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YEREMIYA 8-11
Anthu Angapambane Kokha Ngati Atsogozedwa na Yehova
Anthu sangakwanitse kudzilamulila, ndipo si oyenelela kutelo
10:21-23
Cifukwa cakuti abusa auzimu a Aisiraeli sanali kufunsila kwa Yehova, anthu anamwazikana
Koma amene anatsatila citsogozo ca Yehova anali kukhala mwa mtendele mwa cimwemwe, ndipo zinthu zinali kuwayendela bwino