LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 March tsa. 3
  • March 13-19

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 13-19
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 March tsa. 3

March 13-19

YEREMIYA 5-7

  • Nyimbo 66 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Analeka Kucita Cifunilo ca Mulungu”: (10 min.)

    • Yer. 6:13-15—Yeremiya anavumbula macimo a mtundu wa Aisiraeli (w88 4/1 peji 11-12 mapala. 7-8)

    • Yer. 7:1-7—Yehova anayesa kuwathandiza kuti alape (w88 4/1 peji 12 mapala. 9-10)

    • Yer. 7:8-15—Aisiraeli anali kuona monga Yehova sadzacitapo kanthu (jr peji 21 pala. 12)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Yer. 6:16—Kodi Yehova analimbikitsa anthu ake kucita ciani? (w05 11/1 peji 23 pala. 11)

    • Yer. 6:22, 23—N’cifukwa ciani tingati anthu anali ‘kudzabwela kucokela kudziko la kumpoto’? (w88 4/1 peji 13 pala. 15)

    • Kodi ine pacanga, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino zimene ine pacanga ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Yer. 5:26–6:5

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo) T-36—Yalani maziko a ulendo wobwelelako.

  • Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) T-36—Kambilanani kamutu kakuti “Ganizilani Funso Ili.” Itanilani munthuyo ku Cikumbutso.

  • Phunzilo la Baibo: (6 mineti kapena kucepelapo) jl phunzilo 1—Itanilani munthuyo ku Cikumbutso.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 125

  • “Kuseŵenzetsa Kabuku Kakuti Ndani Amene Akucita Cifunilo ca Yehova Masiku Ano?”: (15 min.) Yambani mwa kufotokoza nkhaniyi kwa 5 mineti. Ndiyeno tambitsani na kukambilana vidiyo yoonetsa mmene tingaseŵenzetsele kabukuka pa phunzilo 8. Limbikitsani onse amene amatsogoza maphunzilo a Baibo kuti aziseŵenzetsa kakubuka wiki iliyonse.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 9 mapala. 16-21, bokosi papeji 94, na bokosi lobwelelamo papeji 95

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 10 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani