LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 March tsa. 6
  • March 27–April 2

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 27–April 2
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 March tsa. 6

March 27–April 2

YEREMIYA 12-16

  • Nyimbo 135 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Aisiraeli Anaiŵala Yehova” (10 min.)

    • Yer. 13:1-5—Yeremiya analabadila malangizo a Yehova a kubisa lamba wansalu, ngakhale kuti sicinali capafupi (jr peji 51 pala. 17)

    • Yer. 13:6, 7—Yeremiya atayenda msenga wautali kukatenga lambayo, anapeza kuti wawonongeka (jr peji 52 pala. 18)

    • Yer. 13:8-11—Yehova anali kuonetsa kuti ubale wolimba umene anali nawo ndi Aisiraeli udzasokonezeka cifukwa ca umbulamatu wawo (jr 52 mapala. 19-20; it-1 peji 1121 pala. 2)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Yer. 12:1, 2, 14—Kodi Yeremiya anafunsa ciani? Nanga Yehova anayankhanji? (jr peji 118 pala. 11)

    • Yer. 15:17—Kodi Yeremiya anali kuwaona bwanji anthu oyanjana nawo? Nanga tingatengele bwanji citsanzo cake? (w04 5/1 peji 12 pala. 16)

    • Kodi ine pacanga, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino zimene ine pacanga ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Yer. 13:15-27

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo) Ciitano ca ku Cikumbutso na kutambitsa vidiyo—Yalani maziko a ulendo wobwelelako.

  • Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) Ciitano ca ku Cikumbutso na kutambitsa vidiyo—Yalani maziko a ulendo wotsatila.

  • Nkhani: (6 min.) w16.03 peji 29-31—Mutu Wake: Ndi liti Pamene Anthu a Mulungu Anali mu Ukapolo kwa Babulo Wamkulu?

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 139

  • “Thandizani a m’Banja Lanu Kukumbukila Yehova”: (15 min.) Kukambilana. Yambani mwa kutambitsa vidiyo yakuti “Mau Awa . . . Azikhala Pamtima Pako”—Kufunsa Mafunso Mabanja (yendani ku mavidiyo BANJA).

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 10 mapala. 8-11, mabokosi pa peji 103, na 105 (kumanzele)

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 48 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani