October 23-29
HOSEYA 8-14
Nyimbo 153 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“M’patseni Zabwino Koposa Yehova”: (10 min.)
Hos. 14:2—Yehova amayamikila kwambili mau otamanda apakamwa pathu (w07 4/1 peji 19, 20 pala. 2
Hos. 14:4—Yehova amakhululukila, kuyanja, na kukhala bwenzi la anthu amene amam’patsa zabwino koposa (w11 2/15 peji 16 pala. 15)
Hos. 14:9—Kuyenda m’njila za Yehova kumatipindulitsa (jd peji 87 pala. 11)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Hos. 10:12—Tifunika kucita ciani kuti tikolole “zipatso za” cikondi cokhulupilika ca Yehova? (w05 11/15 peji 28 pala. 7)
Hos. 11:1—Kodi mau amenewa anakwanilitsika bwanji kwa Yesu? (w11 8/15 peji 10 pala. 10)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Hos. 8:1-14
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo) T-35
Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) T-35—Kapepa kauthenga aka kanagaŵilidwa paulendo woyamba. Pamene mupitiliza makambilanowo mwininyumba atulutse mfundo yotsutsa, koma m’khutilitseni.
Phunzilo la Baibo: (6 mineti kapena kucepelapo) lv peji 152 mapa. 13-15—Onetsani mmene tingam’fikile pamtima wophunzila.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Kukhala na Umoyo Wotamanda Yehova” (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Seŵenzetsani Maluso Anu Kutamanda Nawo Yehova.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 20 mapa. 7-16, bokosi “Cida Cina ca Ogwila Nchito Yopeleka Thandizo”
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 63 na Pemphelo