CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | HOSEYA 8-14
M’patseni Zabwino Koposa Yehova
14:2, 4, 9
Kum’patsa zabwino koposa Yehova kumam’kondweletsa ndipo kumakupindulitsani
UBWENZI WANU NA YEHOVA
Mukapeleka nsembe za citamando kwa Yehova
Yehova adzakukhululukilani, kukuyanjani, na kukhala bwenzi lanu
Mudzapindula cifukwa comvela Yehova, ndipo cifuno canu com’tamanda cidzawonjezeka
Ningam’patse bwanji zabwino koposa Yehova?