LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 November tsa. 4
  • M’patseni Zabwino Koposa Yehova

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • M’patseni Zabwino Koposa Yehova
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Nkhani Zofanana
  • M’patseni Zabwino Koposa Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • “Ine Ndidzakhala Nawe Polankhula”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Zamkatimu
    Galamuka!—2022
  • Kanizani Ziyeso Mmene Yesu Anacitila
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 November tsa. 4
Zithunzi: Yehova anali kulandila nsembe zosiyana-siyana kucokela kwa Aisiraeli. 1. Ufa wosalala. 2. Nkhunda. 3. Banja likupeleka nkhosa kwa wansembe.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LEVITIKO 4-5

M’patseni Zabwino Koposa Yehova

5:5-7, 11

Kusauka sikunalepheletse munthu aliyense mu Isiraeli kukonzanso ubale wake na Yehova. Ngakhale anthu osauka kwambili anali kukwanitsa kupeleka nsembe yovomelezeka kwa Yehova, malinga ngati apeleka zinthu zawo zabwino koposa. Anali kupeleka ufa, koma Yehova anafunabe kuti ufawo ukhale “wosalala,” ngati umene anali kuseŵenzetsa pophikila alendo cakudya. (Gen. 18:6) Masiku anonso, Yehova amalandila nsembe yathu yabwino kwambili yacitamando, ngakhale kuti mwina timalephela kucita zambili cifukwa ca mmene zinthu zilili pa umoyo wathu.—Aheb. 13:15.

Kodi mfundoyi ingakulimbikitseni bwanji ngati simukwanitsa kucita zambili mmene munali kucitila kale, mwina cifukwa ca kufooka kwa thanzi kapena kucepa kwa mphamvu?

Zithunzi: Alongo aŵili akupeleka nsembe yawo yabwino kwambili yacitamando kwa Yehova. 1. Mlongo amene atumikila m’gawo la citundu cina, akukamba na mayi wina pamsika. 2. Mlongo wacikulile akulemba makalata panyumba.
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani