LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 June tsa. 6
  • Kanizani Ziyeso Mmene Yesu Anacitila

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kanizani Ziyeso Mmene Yesu Anacitila
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Nkhani Zofanana
  • Musamakonde Dziko Kapena Zinthu za M’dziko
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Ganizilani Za Mtundu Wa Munthu Amene Muyenela Kukhala
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2013
  • Kondani Cilungamo, Danani Nako Kusamvela Malamulo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • “Mulungu . . . Anamuyesa Abulahamu”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 June tsa. 6

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | LUKA 4-5

Kanizani Ziyeso Mmene Yesu Anacitila

Satana amafuna kuwononga ubwenzi wathu na Yehova mwa kuticititsa kulaka-laka zoipa. Iye amayesa munthu aliyense kulingana na mmene zinthu zilili mu umoyo wake komanso zimene amakonda.

Ni cida camphamvu citi cimene Yesu anaseŵenzetsa kuti asagonje ku mitundu itatu ya ziyeso zimene anakumana nazo? (Aheb. 4:12; 1 Yoh. 2:15, 16) Ningatengele bwanji citsanzo cake?

  • Yesu akukana kusandutsa miyala kuti ikhale mikate

    4:1-4

    “Cilako-lako ca thupi”

  • Yesu akukana ciyeso ca Mdyelekezi pamene akumuonetsa maufumu onse a padziko lapansi

    4:5-8

    “Cilako-lako ca maso”

  • Yesu ali pamwamba pa mpanda wa kacisi

    4:9-12

    “Kudzionetsela”

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani