CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AHEBERI 1-3
Kondani Cilungamo, Danani Nako Kusamvela Malamulo
1:9
Yesu amakonda cilungamo, ndipo amadana na ciliconse cimene cimanyazitsa Atate ŵake.
Tingatengele bwanji citsanzo ca Yesu cokonda cilungamo . . .
tikayesedwa kucita zoipa?
ngati wacibale wathu wacotsedwa mu mpingo?