LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 December tsa. 2
  • Cikondi pa Yehova Ciyenela Kukhala Cacikulu Kuposa Cikondi pa Acibale

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Cikondi pa Yehova Ciyenela Kukhala Cacikulu Kuposa Cikondi pa Acibale
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Tiyenela Kucita Bwanji ndi Munthu Wocotsedwa?
    “Khalanibe m’Cikondi ca Mulungu”
  • Munthu Amene Timakonda Akasiya Yehova
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2021
  • Kondani Cilungamo, Danani Nako Kusamvela Malamulo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Timaonetsa Cikondi Ngati Ticita Zinthu Mogwilizana na Cilango ca Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 December tsa. 2
Mkulu wa ansembe Aroni waimilila m’bwalo la cihema. Asuweni a Aroni aŵili anyamula mitembo ya Nadabu na Abihu pamacila kupita nayo kunja kwa msasa.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LEVITIKO 10-11

Cikondi pa Yehova Ciyenela Kukhala Cacikulu Kuposa Cikondi pa Acibale

10:1, 2, 4-7

Nadabu na Abihu atenga zofukizila zodzala na moto na zofukiza.

Kukhulupilika kwathu kwa Yehova kungayesedwe kwambili ngati munthu amene timakonda wacotsedwa mu mpingo. Malangizo amene Yehova anapatsa Aroni ni cenjezo kwa Akhristu amene amayanjana na wacibale wocotsedwa. Cikondi cathu pa Yehova ciyenela kukhala cacikulu kuposa cikondi cathu pa acibale osakhulupilika.

Kodi Akhristu amene amatsatila malangizo a Yehova ponena za ocotsedwa amalandila madalitso otani? —1 Akor. 5:11; 2 Yoh. 10, 11

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani