CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | ZEKARIYA 1-8
“Adzagwila Covala ca Munthu Amene ndi Myuda”
8:20-23
Amuna 10 ocokela m’zinenelo zonse za anthu adzagwila covala ca Myuda, na kukamba kuti, “anthu inu tipita nanu limodzi.” M’masiku ano otsiliza, anthu ocokela m’mitundu yonse akukhamukila kwa Yehova kuti amulambile pamodzi na Akhristu odzozedwa
Kodi a nkhosa zina masiku ano amathandizila odzozedwa m’njila ziti?
Amagwila nchito yolalikila na mtima wonse
Amacita zopeleka mopanda kaso pothandizila nchitoyi