LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 January tsa. 3
  • January 8-14

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • January 8-14
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 January tsa. 3

January 8-14

MATEYU 4-5

  • Nyimbo 82 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Zimene Tiphunzilapo pa Ulaliki wa Yesu wa pa Phili”: (10 min.)

    • Mat. 5:3—Munthu amakhala wodala ngati azindikila zosoŵa zake zauzimu. (“Odala,” “anthu amene amazindikila zosoŵa zawo zauzimu” mfundo zounikila pa Mat. 5:3 nwtsty)

    • Mat. 5:7—Munthu amakhala wodala ngati ni wacifundo (“acifundo” mfundo younikila pa Mat. 5:7 nwtsty)

    • Mat. 5:9—Munthu amakhala wodala ngati amabweletsa mtendele (“amene amabweletsa mtendele” mfundo younikila pa Mat. 5:9 nwtsty; w07 12/1 peji 17)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Mat. 4:9—Kodi Satana anayesa kunyengelela Yesu kuti acite ciani? (“kuŵelama kamodzi kokha” mfundo younikila pa Mat. 4:9 nwtsty)

    • Mat. 4:23—Ni zinthu ziŵili ziti zofunika zimene Yesu anacita? (“kuphunzitsa . . . kulalikila” mfundo younikila pa Mat. 4:23 nwtsty)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mat. 5:31-48

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Onani Makambilano a Citsanzo.

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Nkhani: (6 min. olo kucepelapo) w16.03 mape. 31-32—Mutu: Pamene Satana Anali Kuyesa Yesu, Kodi Anam’tengela ku Kacisi Weni-weni, Kapena Anangomuonetsa Kacisiyo M’masomphenya Cabe?

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 130

  • Odala ndi Anthu Amene Akuzunzidwa Cifukwa ca Cilungamo: (9 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Banja la M’bale Namgung: Linamangiwa Cifukwa ca Cikhulupililo, ndiyeno kambilanani zimene mwaphunzilapo (pitani pa mavidiyo ZOCITIKA NA KUFUNSA MAFUNSO).

  • “Pita Ukayanjane ndi m’Bale Wako Coyamba—Motani?”: (6 min.) Kukambilana. Kambilanani cifukwa cake kucita zili pa kadoti kothela ndiye kungakhale kofunika.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 3

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 141 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani