January 21-27
MACHITIDWE 25-26
Nyimbo 73 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Paulo Apempha Kukaonekela kwa Kaisara Kenako Alalikila Mfumu Herode Agiripa”: (10 min.)
Mac. 25:11—Paulo anaseŵenzetsa ufulu wake wa lamulo kuti akaonekele kwa Kaisara (bt peji 198 pala. 6)
Mac. 26:1-3—Paulo mwaluso anaikila kumbuyo coonadi pa maso pa Mfumu Herode Agiripa (bt mape. 198-201 mapa. 10-16)
Mac. 26:28—Mfumuyo inakhudzika mtima kwambili na mawu a Paulo (bt peji 202 pala. 18)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Mac. 26:14—Kodi cisonga cotosela n’ciani? (“kuponya miyendo yake kuti imenye zisonga zotosela” nwtsty mfundo younikila; nwt matanthauzo a mawu ena, ‘cisonga cotosela’)
Mac. 26:27—N’cifukwa ciani Mfumu Agiripa anavutika kuyankha Paulo atamufunsa ngati anali kukhulupilila zolemba za aneneli? (03 11/15 mape. 16-17 pala. 14)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mac. 25:1-12 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Kubwelelako Koyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Kubwelelako Koyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 2)
Kubwelelako Koyamba: (4 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani buku lakuti Zimene Baibulo Ingatiphunzitse. (th phunzilo 3)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Kupatsidwa Ufulu Wolalikila ku Quebec”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 51
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 122 na Pemphelo