CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AROMA 1-3 Pitilizani Kuphunzitsa Cikumbumtima Canu 2:14, 15 Cikumbumtima cathu cingatithandize ngati ticiphunzitsa mfundo za m’Baibo ticimvelela cikatikumbutsa mfundo zimenezo tipempha mzimu woyela kuti utithandize kusacita zoipa.—Aroma 9:1