February Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano February 2019 Makambilano Acitsanzo February 4-10 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AROMA 1-3 Pitilizani Kuphunzitsa Cikumbumtima Canu UMOYO WATHU WACIKHRISTU Kodi Mumawaona Makhalidwe Osaoneka a Mulungu? February 11-17 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AROMA 4-6 “Mulungu Akuonetsa Cikondi Cake Kwa Ife” February 18-24 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AROMA 7-8 Kodi Mukuyembekezela Mwacidwi? UMOYO WATHU WACIKHRISTU Pitilizani Kuyembekezela Mopilila February 25–March 3 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AROMA 9-11 Fanizo la Mtengo wa Maolivi UMOYO WATHU WACIKHRISTU Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kuleka Kutsogoza Maphunzilo a Baibo Osapita Patsogolo