CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AROMA 7-8
Kodi Mukuyembekezela Mwacidwi?
“Cilengedwe”: anthu amene ali na ciyembekezo cokakhala padziko lapansi
‘Kuonekela kwa ana a Mulungu’: nthawi pamene odzozedwa adzathandiza Khristu kuwononga dongosolo loipa la Satana
“Maziko a ciyembekezo”: lonjezo la Yehova lotipulumutsa kupitila mu imfa ya Yesu na kuukitsidwa kwake
‘Kumasulidwa ku ukapolo wa kuvunda’: kumasulidwa pang’ono-pang’ono kucoka ku ucimo na imfa