LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 February tsa. 5
  • February 18-24

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • February 18-24
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 February tsa. 5

February 18-24

AROMA 7-8

  • Nyimbo 27 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Mukuyembekezela Mwacidwi?”: (10 min.)

    • Aroma 8:19—Posacedwa “ana a Mulungu” adzaonekela (w12 7/15 peji 11 pala. 17)

    • Aroma 8:20—“Cilengedwe cinapelekedwa ku mkhalidwe wopanda pake . . . pa maziko a ciyembekezo” (w12 3/15 peji 23 pala. 11)

    • Aroma 8:21—Cilengedwe “cidzamasulidwa ku ukapolo wa kuvunda” (w12 3/15 peji 23 pala. 12)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Aroma 8:6—Kodi pali kusiyana kotani pakati pa “kuika maganizo pa zinthu za thupi” na “kuika maganizo pa zinthu za mzimu”? (w17.06 peji 3))

    • Aroma 8:26, 27—Kodi Yehova amayankha bwanji ‘madandaulo amene sitingathe kuwafotokoza’? (w09 11/15 peji 7 pala. 20)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Aroma 7:13-25 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Kubwelelako Koyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Kubwelelako Koyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 6)

  • Kubwelelako Koyamba: (5 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Kenako chulani na kukambilana vidiyo yakuti Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji? (Koma musaitambitse vidiyoyi) (th phunzilo 9)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 139

  • “Pitilizani Kuyembekezela Mopilila”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Tifunika “Kuthamanga Mopilila”—Khalani na Cidalilo Cakuti Mudzalandila Mphoto.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 55

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 124 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani