LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 February tsa. 4
  • February 11-17

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • February 11-17
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 February tsa. 4

February 11-17

AROMA 4-6

  • Nyimbo 20 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mulungu Akuonetsa Cikondi Cake Kwa Ife”: (10 min.)

    • Aroma 5:8, 12—Yehova anationetsa cikondi “pamene tinali ocimwa” (w11 6/15 peji 12 pala. 5)

    • Aroma 5:13, 14—Ucimo na imfa zinalamulila monga mfumu (w11 6/15 peji 12 pala. 6)

    • Aroma 5:18, 21—Yehova anatumiza mwana wake kuti tilandile moyo (w11 6/15 mape. 12-13 mapa. 9-10)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Aroma 6:3-5—Kodi kubatizidwa “mu mgwilizano ndi Khristu Yesu” komanso kubatizidwa “mu imfa yake,” kukutanthauza ciani? (w08 6/15 peji 29 pala. 7)

    • Aroma 6:7—N’cifukwa ciani oukitsidwa sadzaweluzidwa mogwilizana na macimo amene anacita akalibe kufa? (w14 6/1 peji 11 pala. 1)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Aroma 4:1-15 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI]

  • Vidiyo ya Kubwelelako Koyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 4)

  • Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Mukayamba makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko amene anthu amakamba pokana kuwalalikila. Koma muyankheni mwaluso. (th phunzilo 6)

  • Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani cofalitsa cophunzitsila ca mu Thuboksi yathu. (th phunzilo 9)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 107

  • Zofunikila za Mpingo: (15 min.)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 54

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 97 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani