LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 March tsa. 4
  • Kodi Ndimwe Munthu Wakuthupi Kapena Wauzimu?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Ndimwe Munthu Wakuthupi Kapena Wauzimu?
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Nkhani Zofanana
  • Pitani Patsogolo Monga Munthu Wauzimu
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2018
  • Kodi Kukhala Munthu Wauzimu Kumatanthauzanji?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2018
  • Abale Acinyamata, Kodi Mukukalamila?
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Acicepele—Kodi Mukukula Mwauzimu?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 March tsa. 4

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 1 AKORINTO 1-3

Kodi Ndimwe Munthu Wakuthupi Kapena Wauzimu?

2:14-16

Aliyense wa ife afunika kukulitsa uzimu wake na kupitiliza kukhala munthu wauzimu. (Aef. 4:23, 24) Kuti mupite patsogolo mwauzimu, mufunika kudzidyetsa mwauzimu, kudziikila zolinga zauzimu, komanso kukulitsa makhalidwe amene mzimu woyela umabala.

Zosangalatsa, zolinga, komanso makambilano pakati pa munthu wakuthupi na munthu wauzimu

Kodi uzimu wanu pali pano uli bwanji mukauyelekezela na mmene unalili caka catha, zaka 10 zapitazo, kapena pamene munabatizika?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani