LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 September tsa. 2
  • “Wansembe Mpaka Muyaya Monga mwa Unsembe wa Melekizedeki”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Wansembe Mpaka Muyaya Monga mwa Unsembe wa Melekizedeki”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 September tsa. 2
Yesu ali pa mpando wake wacifumu kumwamba, ndipo wanyamula ndodo yacifumu m’manja mwake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AHEBERI 7-8

“Wansembe Mpaka Muyaya Monga mwa Unsembe wa Melekizedeki”

7:1-3, 17

Kodi Melekizedeki anaimila Yesu m’njila ziti?

  • 7:1​—Anali Mfumu komanso Wansembe

  • 7:3, 22-25​—Palibe paliponse m’Baibo pamene paonetsa kuti iye anacita kuloŵa m’malo munthu wina, kapena pamene paonetsa kuti anali na womuloŵa m’malo

  • 7:5, 6, 14-17​—Anacita kusankhidwa na Yehova kukhala wansembe, osati kucita kuutengela kwa makolo ake

Mkulu wa ansembe m’nthawi ya Aisiraeli, wavala covala cake ca unsembe

Kodi unsembe wa Khristu ni wapadela kuposa wa Aroni m’njila yotani? (it-1 1113 ¶4-5)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani