September 9-15
AHEBERI 9-10
Nyimbo 10 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mthunzi wa Zinthu Zabwino Zimene Zikubwela”: (10 min.)
Aheb. 9:12-14—Magazi a Khristu ni amtengo wapatali kuposa a mbuzi kapena a ng’ombe (it-1 862 ¶1)
Aheb. 9:24-26—Khristu anapeleka nsembe ya mtengo wapatali kwa Mulungu kamodzi ku nthawi zonse (cf 183 ¶4)
Aheb. 10:1-4—Cilamulo cinali kucitila cithunzi zinthu zabwino za kutsogolo (it-2 602-603)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Aheb. 9:16, 17—Kodi mavesiwa atanthauza ciani? (w92 3/1 31 ¶4-6)
Aheb. 10:5-7—Ni pa nthawi iti pamene Yesu anakamba mawu amenewa? Nanga anali kutanthauza ciani? (it-1 249-250)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Aheb. 9:1-14 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 1)
Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Mukayamba makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso, loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 2)
Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani kakhadi kongenela pa webusaiti yathu. (th phunzilo 11)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Kodi Timaona Misonkhano Yathu Kukhala Yofunika? (Sal. 27:11): (12 min.) Tambitsani vidiyoyi. Pambuyo pake, kambilanani mafunso aya:
Kodi Mkulu wathu wa Ansembe Yesu, amagwila nchito ziti zimene zimatipindulitsa?
Kodi tingaonetse kuti ndife oyamikila m’njila zitatu ziti?
Uzimvetsela pa Misonkhano: (3 min.) Tambitsani vidiyoyi. Ndiyeno pemphani acicepele kuti afotokoze cifukwa cake afunika kumvetsela mwachelu pa misonkhano.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 83
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 108 na Pemphelo