CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AHEBERI 9-10
“Mthunzi wa Zinthu Zabwino Zimene Zikubwela”
9:12-14, 24-26; 10:1-4
Cihema cinacitila cithunzi makonzedwe amene Mulungu anapanga ophimba macimo athu kupitila mu dipo. Gwilizanitsani mbali zinayi zotsatilazi za cihema, na zimene mbali iliyonse inali kucitila cithunzi.
|
|