September 16-22
AHEBERI 11
Nyimbo 119 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Cifukwa Cake Cikhulupililo N’cofunika”: (10 min.)
Aheb. 11:1—Zimene cikhulupililo cimatanthauza (w16.10 27 ¶6)
Aheb. 11:6—Cikhulupililo n’cofunikila kuti tizikondweletsa Mulungu (w13 11/1 11 ¶2-5)
Aheb. 11:33-38—Cikhulupililo cinathandiza atumiki a Mulungu a kale kupilila mavuto osiyana-siyana (w16.10 23 ¶10-11)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Aheb. 11:4—N’ciani cinathandiza Abele kukhala na cikhulupililo colimba? (it-1 804 ¶5)
Aheb. 11:5—Kodi Inoki anadalitsidwa bwanji pa cikhulupililo cake? (wp17.1 12-13)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Aheb. 11:1-16 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Ulendo Wobwelelako Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 3)
Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Kenako, gaŵilani mwininyumba kapepa koitanila anthu ku misonkhano, na kuchula za vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? (koma musaitambitse) (th phunzilo 11)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Kodi Mudzacita Ciani pa Nthawi ya Cilala?”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 84
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 54 na Pemphelo