CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AHEBERI 11
Cifukwa Cake Cikhulupililo N’cofunika
11:1, 6, 33-38
Kodi kukhala na cikhulupililo colimba kungakuthandizeni bwanji m’zocitika zotsatilazi?
Mukauzidwa kucita utumiki umene muona kuti ni wovuta.—Aheb. 11:8-10
Pamene mwatayikilidwa wokondedwa wanu mu imfa—Aheb. 11:17-19
Ngati boma lakulandani ufulu pankhani yolambila.—Aheb. 11:23-26