LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 January tsa. 3
  • Kodi Mungafotokoze Cikhulupililo Canu?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Mungafotokoze Cikhulupililo Canu?
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Nkhani Zofanana
  • Phunzilani Zambili za Yehova Poyang’ana Cilengedwe Cake
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
  • Wacicepele, Limbitsa Cikhulupililo Cako
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2016
  • Limbitsani Cikhulupililo Canu mwa Mlengi
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2021
  • Mmene Cilengedwe Cimaonetsela Cikondi ca Mulungu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 January tsa. 3
M’bale akuŵelengela munthu lemba m’Baibo ku nchito kwawo pa nthawi yopumula masana.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Kodi Mungafotokoze Cikhulupililo Canu?

Ngati munthu wakufunsani cifukwa cake mumakhulupilila kuti Mulungu ndiye analenga zinthu zonse, mungamuyankhe bwanji? Kuti mumuyankhe mwa cidalilo, mufunika kucita zinthu ziŵili: Coyamba , mufunika kupeza umboni wokukhutilitsani inumwini wakuti zinthu zinacita kulengedwa. (Aroma 12:1, 2) Caciŵili, mufunika kudziŵa mmene mungafotokozele munthu wina zimene mumakhulupilila.​—Miy. 15:28.

TAMBITSANI VIDIYO YAKUTI DOKOTA WOONA ZA MAFUPA AFOTOKOZA CIKHULUPILILO CAKE, KOMANSO YAKUTI KATSWILI WA ZA NYAMA AFOTOKOZA CIKHULUPILILO CAKE, KUTI MUONE ZIFUKWA ZIMENE ENA ALI NAZO ZOKHULUPILILA KUTI ZINTHU ZINACITA KULENGEDWA, NDIYENO KAMBILANANI MAFUNSO AYA:

  • [Cithunzi papeji 3]

    N’cifukwa ciani Irène Hof Laurenceau amakhulupilila kuti zinthu zinacita kulengedwa m’malo mokhulupilila za cisanduliko?

  • Yaroslav Dovhanych.

    N’cifukwa ciani Yaroslav Dovhanych amakhulupilila kuti zinthu zinacita kulengedwa m’malo mokhulupilila za cisanduliko?

  • Kodi mungamufotokozele bwanji munthu wina cifukwa cake mumakhulupilila kuti zinthu zinacita kulengedwa?

  • Ni zofalitsa ziti za m’gulu la Yehova zimene muli nazo m’citundu canu, zimene zingakuthandizeni imwe na anthu ena kupeza maumboni oonetsa kuti Mulungu ndiye analenga zinthu zonse?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani