LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 April tsa. 5
  • April 20-26

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • April 20-26
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 April tsa. 5

April 20-26

GENESIS 32-33

  • Nyimbo 21 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Mukulimbikila kuti Mupeze Madalitso?”: (10 min.)

    • Gen. 32:24—Yakobo anagwebana na mngelo (w03 8/15 25 ¶3)

    • Gen. 32:25, 26—Yakobo sanaleke kugwebana na mngeloyo kufikila atadalitsidwa (it-2 190)

    • Gen. 32:27, 28—Yakobo anadalitsidwa cifukwa ca kulimbikila kwake (it-1 1228)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)

    • Gen. 32:11, 13-15—Tingatengele bwanji khama la Yakobo pa nkhani yokhazikitsa mtendele? (w10 6/15 22 ¶10-11)

    • Gen. 33:20—N’cifukwa ciani Yakobo anacha guwa lansembe “Mulungu, Mulungu wa Isiraeli”? (it-1 980)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova Mulungu, ulaliki, kapena mbali ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Gen. 32:1-21 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi. Kenako funsani omvetsela mafunso aya: Kodi Elise wacita ciani kuti alalikile molondola komanso mokhulutilitsa? Kodi Elise na Morgan athandizana bwanji polalikila?

  • Ulendo Wobwelelako Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 12)

  • Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno chulani na kukambilana vidiyo yakuti Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji? (koma musaitambitse) (th phunzilo 16)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 35

  • “Kodi Cofunika Koposa kwa Ine N’ciani?”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Sumikani Maganizo pa Zolinga Zauzimu.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 111 ¶10-21

  • Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)

  • Nyimbo 150 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani