LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 June tsa. 6
  • “Ndidzakhala Amene Ndidzafune Kukhala”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Ndidzakhala Amene Ndidzafune Kukhala”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Nkhani Zofanana
  • Inu Abale Acinyamata​—Khalani Amuna Okhwima Mwauzimu
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
  • Zamkatimu
    Galamuka!—2022
  • “Ine Ndidzakhala Nawe Polankhula”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • M’kope Ino ya Galamuka!
    Galamuka!—2022
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 June tsa. 6
Mose wagwada pansi ndipo wabisa nkhope yake ku citsamba coyaka moto.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKSODO 1-3

“Ndidzakhala Amene Ndidzafune Kukhala”

3:13, 14

Yehova anafotokozela Mose mbali yocititsa cidwi yokhudza umunthu wake. Amakhala aliyense amene angafunike kukhala pa cocitika ciliconse kuti akwanilitse cifunilo cake mosapitilila miyezo yake yolungama. Mofanana na makolo athu, Yehova amatenga udindo uliwonse wofunikila kuti asamalile ana ake.

Kodi Yehova watenga maudindo otani ponisamalila mu umoyo wanga?

Zithunzi: Tate asamalila banja lake m’njila zosiyana-siyana. 1. Akamba na mwana wake asanagone. 2. Acita lemba latsiku na mkazi wake komanso mwana wawo wamwamuna. 3. Aphunzitsa mwana wake njinga.
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani