June 29–July 5
EKSODO 4-5
Nyimbo 3 na Pemphelo
Mawu Oyamba (1 min.)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Ine Ndidzakhala Nawe Polankhula”: (10 min.)
Eks. 4:10, 13—Mose anaona kuti sangaikwanitse nchito imene anapatsidwa (w10 10/15 13-14)
Eks. 4:11, 12—Yehova anam’tsimikizila kuti adzam’thandiza (w14 4/15 9 ¶5-6)
Eks. 4:14, 15—Yehova anapeleka Aroni kuti athandize Mose (w10 10/15 14)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)
Eks. 4:24-26—Cingakhale cifukwa citi cimene cinapangitsa Zipora kuchula Yehova kuti “mkwati wa magazi”? (w04 3/15 28 ¶4)
Eks. 5:2—Kodi Farao anatanthauza ciani pamene anakamba kuti sam’dziŵa Yehova? (it-2 12 ¶5)
Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova Mulungu, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Eks. 4:1-17 (th phunzilo 12)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo, ndiyeno itanilani munthuyo ku misonkhano yathu. (th phunzilo 2)
Ulendo Wobwelelako: (4 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo, ndiyeno gaŵilani cofalitsa cophunzitsila Baibo. (th phunzilo 4)
Phunzilo la Baibo: (5 min. olo kucepelapo) bhs 100 ¶15-16 (th phunzilo 8)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Moseŵenzetsela Makambilano Acitsanzo”: (5 min.) Kukambilana.
“Mungakwanitse Kulalikila na kuphunzitsa!”: (10 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Khalani Olimba Mtima . . . Inu Ofalitsa.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 121
Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)
Nyimbo 73 na Pemphelo