July 27–August 2
EKSODO 12
Nyimbo 20 na Pemphelo
Mawu Oyamba (1 min.)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mwambo wa Pasika—Zimene Umatanthauza kwa Akhristu”: (10 min.)
Eks. 12:5-7—Zimene mwana wa nkhosa wocitila Pasika anali kuimila (w07 1/1 20 ¶4)
Eks. 12:12, 13—Zimene kuwaza magazi pa khomo kunali kutanthauza (it-2 583 ¶6)
Eks. 12:24-27—Zimene tiphunzilapo pa mwambo wa Pasika (w13 12/15 20 ¶13-14)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)
Eks. 12:12—Kodi ni motani mmene milili kwa Aiguputo, maka-maka wa namba 10, unali ciweluzo kwa milungu yawo yonama? (it-2 582 ¶2)
Eks. 12:14-16—N’ciani cinali capadela na Cikondwelelo ca Mikate Yopanda Cofufumitsa komanso misonkhano ina yopatulika? Nanga inali kuŵapindulitsa motani Aisiraeli? (it-1 504 ¶1)
Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova Mulungu, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Eks. 12:1-20 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Mukayamba makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso, kopani cidwi cake. (th phunzilo 2)
Ulendo Wobwelelako: (4 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo, ndiyeno gaŵilani magazini yaposacedwa yogwilizana na nkhani imene mwakambilana. (th phunzilo 6)
Phunzilo la Baibo: (5 min. olo kucepelapo) bhs 16 ¶21-22 (th phunzilo 19)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Yehova Amateteza Anthu Ake”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kuyendela Miziyamu ya ku Warwick: “Anthu Odziŵika na Dzina la Yehova”.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 125
Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)
Nyimbo 129 na Pemphelo