July Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano, ka July 2020 Makambilano Acitsanzo July 6-12 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKSODO 6–7 “Tsopano Uona Zimene Ndicite kwa Farao” July 13-19 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKSODO 8-9 Farao Wonyadayo Mosadziŵa Anathandiza kuti Cifunilo ca Mulungu Cikwanilitsidwe UMOYO WATHU WACIKHRISTU Khalani Wodzicepetsa—Pewani Kudzitamandila UMOYO WATHU WACIKHRISTU Khalani Wodzicepetsa Ena Akakutamandani July 20-26 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKSODO 10-11 Mose na Aroni aonetsa kulimba kwambili UMOYO WATHU WACIKHRISTU Kodi Zolengedwa Zimatiphunzitsa Ciani za Kulimba Mtima? July 27–August 2, 2020 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKSODO 12 Mwambo wa Pasika—Zimene Umatanthauza kwa Akhristu UMOYO WATHU WACIKHRISTU Yehova Amateteza Anthu Ake