Mose na Aroni acita zozizwitsa pamaso pa Farao
Makambilano Acitsanzo
●○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Tidziŵa bwanji kuti mavuto amene timakumana nawo si cilango cocokela kwa Mulungu?
Lemba: Yak. 1:13
Ulalo: N’cifukwa ciani timavutika?
○● ULENDO WOBWELELAKO
Funso: N’cifukwa ciani timavutika?
Lemba: 1 Yoh. 5:19
Ulalo: Kodi Mulungu amamvela bwanji akaona kuti tikuvutika?