LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 November tsa. 13
  • Yefita Anali Munthu Wauzimu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yefita Anali Munthu Wauzimu
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Mulungu Amakonda Anthu Okhulupilika
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2016
  • Anakondweletsa Atate Wake ndi Yehova
    Phunzitsani Ana Anu
  • Lonjezo La Yefita
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
  • Lonjezo la Yefita
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 November tsa. 13

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yefita​—Anali Munthu Wauzimu

Yefita sanasungile ena cakukhosi (Ower. 11:5-9; w16.04 7 ¶9)

Yefita anaphunzilapo kanthu pa zimene Yehova anacitila anthu ake (Ower. 11:12-15; it-2 27 ¶2)

Yefita anasumika maganizo ake pa nkhani yofunika kwambili, yakuti Yehova ndiye Mulungu woona (Ower. 11:23, 24, 27; it-2 27 ¶3)

Zithunzi: 1. M’bale akuŵelenga Baibo. 2. M’bale akukambilana na mkazi wake mwacikondi. 3. Mwaulemu, mwamuna na mkazi wake akhalabe pansi pamene ena aimilila kuti acitile saliyuti mbendela.

Kodi nimaonetsa m’njila ziti kuti ndine munthu wauzimu?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani