LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsa. 15
  • Pezani Cimwemwe Poyambitsa Makambilano

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Pezani Cimwemwe Poyambitsa Makambilano
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Zisankho Zimene Zimaonetsa Kuti Timadalila Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Anthu a “Maganizo Abwino” Adzalola Kuphunzira Nao
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2025
  • Lembani Mmene Mwapitila Patsogolo
    Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa
  • Muzivomeleza Kuti Pali Zimene Simudziwa
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2025
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 May tsa. 15

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Pezani Cimwemwe Poyambitsa Makambilano

Kuceza na anthu kuti tiwalalikile mwamwayi ni imodzi mwa njila zosangalatsa kwambili komanso zogwila mtima zocitila umboni. Ngakhale n’telo, tingacite mantha kuyambitsa makambilano ngati tiganizila kwambili za mmene tingaloŵetselepo mfundo ya m’Baibo. M’malo modela nkhawa kuti mukamba naye ciyani munthu pomulalikila, ganizilani kwambili mmene mungamuonetsele cidwi. (Mat. 22:39; Afil. 2:4) Ngati pamene mukambilana, mpata wapezeka wakuti mumuuzeko za cikhulupililo canu, pali zida zambili zimene zingakuthandizeni.

Kodi zida zotsatilazi zingakuthandizeni bwanji kuti mulalikile pankhani imene yayambika poceza na munthu?

Tumakadi toloŵela pa JW.ORG.
Cizindikilo ca jw.org.
Zithunzi: Mathilakiti osiyanasiyana. 1. “Kodi Baibo Mumaiona Bwanji?” 2. “Kodi Zinthu Zidzakhala Bwanji Mtsogolo?” 3. “Kodi Cofunika N’ciani Kuti Banja Likhale Lamtendele?” 4. “Kodi Ndani Maka-maka Amene Akulamulila Dzikoli?” 5. “Kodi Mavuto Adzathadi?” 6. “Kodi N’zoona Kuti Akufa Angakhalenso ndi Moyo?” 7. “Kodi Ufumu wa Mulungu ndi Ciani?” 8. “Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambili Onena za Umoyo?”

TAMBANI VIDIYO YAKUTI “CITSULO CIMANOLA CITSULO CINZAKE” —KUYAMBITSA MAKAMBILANO, KENAKO YANKHANI FUNSO ILI:

Ni mfundo zitatu ziti zimene zingatithandize kukulitsa luso lokambilana na anthu?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani