LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsa. 14
  • Khalani Wokhulupilika kwa Yehova Posankha Mabwenzi

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Khalani Wokhulupilika kwa Yehova Posankha Mabwenzi
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Zimene Tikuphunzila m’Buku la Nehemiya
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Mwapatulidwa
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2013
  • Muzilimbikitsa Ena pa Nthawi Zovuta
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • “Cimwemwe Cimene Yehova Amapeleka Ndico Malo Anu Acitetezo”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 July tsa. 14
Nehemiya akutaya katundu wa Tobia kunja kwa cipinda codyelamo ca pakacisi.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Khalani Wokhulupilika kwa Yehova Posankha Mabwenzi

Aamoni na Amowabu sanali kuloledwa “kubwela mumpingo” wa Mulungu cifukwa kale anali kulimbana na anthu a Mulungu (Neh. 13:1, 2; it-1 95 ¶5)

Mkulu wa Ansembe Eliyasibu analola Mwamoni kugwilitsa nchito cipinda codyela ca m’kacisi (Neh. 13:4, 5; w13 8/1 9 ¶5-6)

Nehemiya anaonetsa kukhulupilika kwake kwa Yehova mwa kuthetsa mgwilizano umene Eliyasibu anapanga na mdani wa Mulungu (Neh. 13:7-9)

Kodi tingaonetse kuti ndife okhulupilika kwa Yehova ngati tisankha mabwenzi amene samukonda?—w96 3/15 16 ¶6.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi Yehova amamva bwanji poona mabwenzi amene nimasankha?’

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani