LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • g20 na. 2 tsa. 16
  • Thandizo Ilipo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Thandizo Ilipo
  • Galamuka!—2020
  • Nkhani Zofanana
  • 12 Zolinga
    Galamuka!—2018
  • Pezani Nzelu Zothandiza pa Umoyo pa JW.ORG
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Malangizo Owonjezela kwa Makolo
    Galamuka!—2019
  • Colinga ca Webu Saiti Yathu Ndi Kuthandiza Ife ndi Anthu Ena
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2012
Onaninso Zina
Galamuka!—2020
g20 na. 2 tsa. 16
Mzimayi wakhala pampando wa sofa, ndipo akuŵelenga Baibo.

Thandizo Ilipo

Kodi munthu amene mumam’konda anamwalila?

  • Yendani pa jw.org, na kufufuza mawu akuti “Thandizo Kwa Ofedwa.”

Kodi mumakumana na mavuto azacuma?

  • Yendani pa jw.org, na kufufuza mawu akuti “moseŵenzetsela ndalama.”

Kodi munadzifunsapo kuti, ‘Kodi kukhala na moyo kuli na phindu kwa ine?’

  • Yendani pa jw.org, na kufufuza mawu akuti “mukafika pakuti simufunanso kukhala na moyo” komanso akuti “kodi moyo ukali na phindu kwa ine?”

Kodi mulimbana na matenda osacilitsika?

  • Yendani pa jw.org, na kufufuza mawu akuti “munthu amene mukonda akadwala matenda osacilitsika.”

Baibo imapeleka malangizo opindulitsa kwambili kwa aliyense m’banja. Ndipo mfundo zake zimathandiza munthu kukhala woganiza bwino, komanso kupanga zosankha zanzelu.—MIYAMBO 1:1-4.

Tikupemphani kuti mudziŵelengele mwekha Baibo. Tambani vidiyo yakuti, N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo?.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani