LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • g21 na. 3 tsa. 16
  • Pendani Umboni

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Pendani Umboni
  • Galamuka!—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Thandizani Ana Anu Kukhala na Cikhulupililo Colimba mwa Mlengi Wawo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Kodi Moyo Unayamba Bwanji?
    Kondwelani Na Moyo Kwamuyaya!—Maphunzilo a Baibo Okambilana Komanso Zocita
  • Limbitsani Cikhulupililo Canu mwa Mlengi
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2021
  • Mmene Tingagwilitsile Nchito Kabuku Kakuti Uthenga Wabwino Wocokela kwa Mulungu!
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
Onaninso Zina
Galamuka!—2021
g21 na. 3 tsa. 16
Mnyamata ali pa tebulo m’laibulale; akuŵelenga bulosha yakuti “Kodi Zamoyo Zinachita Kulengedwa?”

Pendani Umboni

Magazini ino ya Galamuka! ifotokoza maumboni ena oonetsa kuti zam’cilengedwe zinacita kulengedwa. Pendani nokha umboni umenewu na kuona ngati pali cifukwa cokhulupilila kuti kuli Mlengi. Pansipa pachulidwa mavidiyo na mabulosha ena amene angakuthandizeni kudziŵa zambili. Mungafufuze mitu yake pa jw.org, ku Chichewa:

N’cifukwa ciani anthu ambili ophunzila amakhulupilila kuti kuli Mlengi?

Onelelani mavidiyo amene ali pa mbali yakuti “Mmene Moyo Unayambira.”

Kodi ciphunzitso cakuti zinthu zinacita kusandulika n’cozikidwa pa mfundo zoona?

Ŵelengani bulosha yakuti Kodi Zamoyo Zinachita Kulengedwa?

Kodi n’canzelu kukhulupilila kuti kuli Mlengi?

Onelelani vidiyo yakuti Zimene Acicepele Anzanu Amakamba—Kukhulupilila mwa Mulungu.

Kodi n’canzelu kukhulupilila Baibo?

Ŵelengani bulosha yakuti Mmene Moyo Unayambira—Mafunso 5 Ofunika Kwambiri.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani