LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 21
  • Anthu Achifundo Amakhala Odala

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Anthu Achifundo Amakhala Odala
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Timatumikila Mulungu “Wacifundo Coculuka”
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2021
  • ‘Acifundo ni Acimwemwe!’
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
Imbirani Yehova
sn nyimbo 21

Nyimbo 21

Anthu Achifundo Amakhala Odala

(Mateyo 5:7)

1. Achifundo ndi odala

Kwa M’lungu ndi okongola.

Amauza ’nthu abwino

Kuti akhale n’chifundo.

M’lungu popereka dipo

Anasonyeza chifundo.

Chifukwatu amadziwa

Kuti ndife ofooka.

2. Achifundo ndi odala

Adzawakhululukira.

Kuti zikhale zotheka

Dipo linaperekedwa.

Timasonyeza chifundo

Pofalitsa uthengawo:

“Sangalalani chifukwa

Ufumu wake wayamba.”

3. Yehova pa chiweruzo

Adzachitira chifundo

Onse omwe ndi ofatsa

Poti amamutsanzira.

Chotero tiziyesetsa

Chifundo kuchikulitsa.

Monga Mulungu ndi Yesu,

Chifundo tisonyezetu.

(Onaninso Luka 6:36; Aroma 12:8; Yak. 2:13.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani