LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 111
  • Iye Adzaitana

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Iye Adzaitana
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Adzaitana
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Mulungu Watilonjeza Moyo Wosatha
    Imbirani Yehova
  • Lonjezo la Moyo Wamuyaya
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Mulungu Watilonjeza Paradaiso
    Imbirani Yehova
Onaninso Zina
Imbirani Yehova
sn nyimbo 111

Nyimbo 111

Iye Adzaitana

(Yobu 14:13-15)

1. Moyo wathu uli ngati nkhungu,

Mwamsanga umapita.

Mu kanthawi kochepa kwambiri

Tingayambe kulira.

Kodi akufa angadzukenso?

M’lungu akulonjeza:

(KOLASI)

Iye adzawaitana

Akufa adzayankha.

Ntchito yamanja ake

Adzailakalaka.

Choncho khulupirirani

M’lungu adzatidzutsa

Mongadi anthu ake.

Tidzakhala kosatha.

2. Anthu a M’lungu angamwalire

Koma saiwalidwa.

Omwe M’lungu akukumbukira

Onse adzadzutsidwa.

Ndipo ife tidzasangalala

Ndi moyo wamuyaya.

(KOLASI)

Iye adzawaitana

Akufa adzayankha.

Ntchito yamanja ake

Adzailakalaka.

Choncho khulupirirani

M’lungu adzatidzutsa

Mongadi anthu ake.

Tidzakhala kosatha.

(Onaninso Yoh. 6:40; 11:11, 43; Yak. 4:14.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani