LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 121
  • Tizilimbikitsana

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Tizilimbikitsana
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Tilimbikitsane Wina na Mnzake
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • “Pitilizani Kutonthozana ndi Kulimbikitsana”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Khalanibe M’cikondi ca Mulungu
    Zimene Baibo Imaphunzitsa M’ceni-ceni
  • “Tiyeni Tilimbikitsane, Ndipo Tiwonjezele Kucita Zimenezi”
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2018
Onaninso Zina
Imbirani Yehova
sn nyimbo 121

Nyimbo 121

Tizilimbikitsana

(Aheberi 10:24, 25)

1. Pomwe timalimbikitsana

Kutumikira Yehova

Timakhaladi okondana

Komanso ogwirizana.

Chikondi cha anthu a M’lungu

Chimatipatsadi mphamvu.

Kumene tingatetezeke

Ndi mkati mwa mpingo wathu.

2. Mawu ochoka kwa abale

A pa nthawi yoyenera

Ndi olimbikitsa kwambiri

Ndipo amatitonthoza.

Kugwirira ntchito limodzi

Ndithu ndikosangalatsa,

Timafuna kuthandizana

Ndi kumalimbikitsana.

3. Popeza tsiku la Yehova

Layandikira kwambiri

Ndikofunika tisaleke

Kusonkhanatu pamodzi.

Tikufuna kutumikira

Ndi abale kwamuyaya.

Choncho ndi njira yachikondi

Kuti tizithandizana.

(Onaninso Luka 22:32; Mac. 14:21, 22; Agal. 6:2; 1 Ates. 5:14.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani