LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • ll gao 12 masa. 26-27
  • Mungacite Ciani Kuti Banja Likhale Lokondweletsa?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mungacite Ciani Kuti Banja Likhale Lokondweletsa?
  • Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya
  • Nkhani Zofanana
  • Mmene Banja Lanu Lingakhalile Lacimwemwe
    Zimene Baibulo Ingatiphunzitse
  • Gao 12
    Mvetselani kwa Mulungu
  • Kodi Muyenela Kucita Ciyani Kuti Banja Lanu Likhale Lacimwemwe?—Mbali 1
    Kondwelani Na Moyo Kwamuyaya!—Maphunzilo a Baibo Okambilana Komanso Zocita
  • Nzelu Zotithandiza Kukhala na Banja Lacimwemwe
    Galamuka!—2021
Onaninso Zina
Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya
ll gao 12 masa. 26-27

GAO 12

Mungacite Ciani Kuti Banja Likhale Lokondweletsa?

Cikondi cimafunika kuti mabanja akhale acimwemwe. Aefeso 5:33

Adamu na Hava m’munda wa Edeni

Lamulo la Mulungu ndi lakuti cikwati ni ca mwamuna mmodzi ndi mkazi mmodzi.

Mwamuna asamalila mkazi wake wodwala; mkazi waphikila mwamuna wake cakudya

Mwamuna wacikondi amacitila cifundo mkazi wake ndipo amamumvetsetsa.

Mkazi ayenela kugwilizana ndi mwamuna wake.

Atate alimbikitsa mwana wawo wamwamuna kumvetsela pa msonkhano wacikhristu

Ana ayenela kumvela makolo ao.

Khalani okoma mtima ndi okhulupilika, osati ankhanza ndi osakhulupilika. Akolose 3:​5, 8-10

Makolo aphunzitsa Baibo mwana wawo wamkazi

Mau a Mulungu amakamba kuti mwamuna ayenela kukonda mkazi wake monga thupi lake ndi kuti mkazi ayenela kulemekeza kwambili mwamuna wake.

Mkazi wakhumudwa pamene mwamuna wake ayang’ana mkazi wina momukhumbila

Kugonana ndi munthu amene simunakwatilane naye ni kulakwa. Kukwatila cipali nako ni kulakwa.

Banja liyang’ana dzuŵa pamene liloŵa

Mau a Yehova amaphunzitsa mabanja mmene angakhalile okondwela.

  • Khalani ndi makhalidwe abwino.—1 Akorinto 6:18.

  • Muzikonda ana anu, muziwaphunzitsa, ndi kuwachinjiliza.—Deuteronomo 6:4-9.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani