Phunzilo 3
1 Petulo 3:8
Davide amva kuti mnzake wadwala.
Conco akamba kuti: “Nidziŵa zimene nidzacita.
Nidzamulembela kalata kuti nimulimbikitse, ndiyeno nidzamupelekela.”
Ukaonetsa kukoma mtima, mnzako adzakondwela.
ZOCITA
Muŵelengeleni mwana wanu:
1 Petulo 3:8
Uzani mwana wanu kuti aloze:
Nyumba Deski Davide
Dzuŵa Mbalame Mtengo
M’funseni mwana wanu:
Kodi udziŵako munthu wina amene adwala?
Tingamulimbikitse bwanji munthuyo?
[Cithunzi 8]
[Cithunzi 8]
[Cithunzi 9]
[Cithunzi 9]