Nyimbo 142
Tilalikile kwa Anthu a Makhalidwe Onse
(1 Timoteyo 2:4)
Tikhale anthu osakondela.
Tikhale monga Mulungu wathu.
Afuna onse apulumuke
Na kukhala atumiki ake.
(KOLASI)
Si malo koma munthu;
Si nkhope koma mtima.
Tiuze anthu onse co’nadi.
Timasakila anthu,
Amene amafuna:
“Kukhala mabwenzi a Yehova.”
Si kanthu mmene aonekela.
Si kanthu kumene acokela.
Mtima wawo ndiwo wofunika—
Ni umene Yehova aona.
(KOLASI)
Si malo koma munthu;
Si nkhope koma mtima.
Tiuze anthu onse co’nadi.
Timasakila anthu,
Amene amafuna:
“Kukhala mabwenzi a Yehova.”
Yehova amalandila onse
Ofuna kukhala anthu ake.
Tilalikile kwa anthu onse.
Tiŵauze uthenga wabwino.
(KOLASI)
Si malo koma munthu;
Si nkhope koma mtima.
Tiuze anthu onse co’nadi.
Timasakila anthu,
Amene amafuna:
“Kukhala mabwenzi a Yehova.”
(Onaninso Yoh. 12:32; Mac. 10:34; 1 Tim. 4:10; Tito 2:11.)