LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 62
  • Nyimbo Yatsopano

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Nyimbo Yatsopano
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Nyimbo Yatsopano
    Imbirani Yehova
  • Moyo Wosatha Watheka!
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Munapeleka Mwana Wanu Wobadwa Yekha
    Imbilani Yehova—Nyimbo Zatsopano
  • Tidzapeza Moyo Wosatha!
    Imbirani Yehova
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 62

NYIMBO 62

Nyimbo Yatsopano

Yopulinta

(Salimo 98)

  1. 1. Imbani nyimbo, Yatsopano kwa Yehova.

    Dziŵitsani onse nchito zake zonse.

    Mutamandeni, lengezani mphamvu zake.

    Poweluza anthu

    ni wacilungamo.

    (KOLASI)

    Imbani!

    Nyimbo yatsopano!

    Imbani!

    Yehova ni Mfumu.

  2. 2. Sangalalani, Lambilani Mfumu yathu!

    Ndipo lengezani ucifumu wake.

    Sekelelani, muimbileni momveka.

    Dziŵitsani dzina lake

    konse-konse.

    (KOLASI)

    Imbani!

    Nyimbo yatsopano!

    Imbani!

    Yehova ni Mfumu.

  3. 3. Zonse za moyo, Zimuimbile mokondwa.

    Mapili na mtunda zitamande M’lungu.

    Onse adziŵe kuti Yehova ni Mfumu

    Cilengedwe conse

    cim’tamande iye.

    (KOLASI)

    Imbani!

    Nyimbo yatsopano!

    Imbani!

    Yehova ni Mfumu.

(Onaninso Sal. 96:1; 149:1; Yes. 42:10.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani