LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 132
  • Lomba Ndise Thupi Limodzi

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Lomba Ndise Thupi Limodzi
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Tsopano Ndife Thupi Limodzi
    Imbirani Yehova
  • Khalani ndi Moyo Wopambana
    Imbirani Yehova
  • Moyo Ndi Wodabwitsa
    Imbirani Yehova
  • Moyo ni Cozizwitsa
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 132

NYIMBO 132

Lomba Ndise Thupi Limodzi

Yopulinta

(Genesis 2:23, 24)

  1. 1. Ine lomba namupeza

    Wonikonda na mtima wonse.

    Ni Yehova wanipatsa,

    Wokondeka wanga.

    Iwe ine; ndise banja,

    Tikondane tisamalane.

    Mu umoyo wathu wonse

    Tidzatumikila Yehova mokhulupilika.

    Tidzakondana

    Na cikondi coona.

    Nalumbila, nalonjeza,

    Nidzakukonda mpaka imfa.

    Tilemekeze Yehova,

    Iye watipatsa banja.

(Onaninso Gen. 29:18; Mlal. 4:9, 10; 1 Akor. 13:8.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani