LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 141
  • Moyo ni Cozizwitsa

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Moyo ni Cozizwitsa
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Moyo Ndi Wodabwitsa
    Imbirani Yehova
  • Khalani ndi Moyo Wopambana
    Imbirani Yehova
  • Umoyo wa Mpainiya
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Umoyo wa Mpainiya
    Imbilani Yehova—Nyimbo Zatsopano
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 141

NYIMBO 141

Moyo ni Cozizwitsa

Yopulinta

(Salimo 36:9)

  1. 1. Yehova M’lungu amatipatsa,

    Mphatso zotithandiza mu umoyo—

    Dzuŵa na mvula, mwana wobadwa.

    Zonse ni mphatso Yehova atipatsa.

    (KOLASI)

    Timayamikila mphatso ya moyo

    Na kukondanso amene anatipatsa.

    Mphatsoyi ya moyo niyodabwitsadi.

    Inde, mphatso iyi—niyapadeladi.

  2. 2. Tikavutika tingaganize

    Kuti moyo ulibe tanthauzo.

    Koma tidziŵa moyo ni mphatso.

    Tiyamikila kuti tili na moyo.

    (KOLASI)

    Timayamikila mphatso ya moyo.

    Timaonetsanso cikondi kwa anzathu.

    Mphatsoyi ya moyo niyodabwitsadi.

    Inde mphatso iyi—niyapadeladi.

(Onaninso Yobu 2:9; Sal. 34:12; Mlal. 8:15; Mat. 22:37-40; Aroma 6:23)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani