Msonkhano wa Dela wa Mboni za Yehova
Pulogilamu ya 2016-2017
Mutu: Pitilizani Kum’konda Yehova —Mat. 22:37.
Cigawo ca Kum’mawa
8:40 Nyimbo Zamalimba
8:50 Nyimbo Na. 50 na Pemphelo
9:00 Muzikumbukila Lamulo Lalikulu Kwambili
9:15 Muzikonda Mulungu, Osati Dziko
9:30 Phunzitsani Ena ‘Kukonda Dzina la Yehova’
9:55 Nyimbo Na. 112 na Zilengezo
10:05 “Munthu Amene Amakonda Mulungu Azikondanso M’bale Wake”
10:35 Kudzipeleka na Ubatizo
11:05 Nyimbo Na. 34
Cigawo ca Kumasana
12:20 Nyimbo Zamalimba
12:30 Nyimbo Na. 73
12:35 Zocitika mu Ulaliki
12:45 Cidule ca Nsanja ya Mlonda
13:15 Makolo—Phunzitsani Ana Anu Kukonda Yehova
13:30 Acicepele—Onetsani kuti Yehova Ni Bwenzi Lanu la Pamtima
13:45 Nyimbo Na. 106 na Zilengezo
13:55 Musasiye ‘Cikondi Cimene Munali Naco Poyamba’
14:55 Nyimbo Na. 3 na Pemphelo
Pezani Mayankho pa Mafunso Aya:
1. Kodi lamulo lalikulu ndi liti? Nanga n’cifukwa ciani n’lofunika kwambili? (Mat. 22:37, 38; Maliko 12:30)
2. Kodi tingapewe bwanji mtima wokonda dziko? (1 Yoh. 2:15-17)
3. Kodi tingawaphunzitse bwanji ena ‘kukonda dzina la Yehova’? (Yes. 56:6, 7)
4. Tingaonetse bwanji cikondi copanda cinyengo kwa abale athu? (1 Yoh. 4:21)
5. Kodi makolo angaphunzitse bwanji ana awo kukonda Yehova? (Deut. 6:4-9)
6. Mungaonetse bwanji kuti Yehova ni Bwenzi lanu la pamtima? (1 Yoh. 5:3)
7. Tingacite ciani kuti tipitilize kukonda Yehova, nanga n’ciani cingatithandize kuyambilanso kumukonda ngati cikondico cinazilala? (Chiv. 2:4, 5)