Tsiku Loyamba
“Tisaleke kucita zabwino” —AGALATIYA 6:9
KUM’MAŴA
8:20 Nyimbo za Pavidiyo
8:30 Nyimbo 143 na Pemphelo
8:40 NKHANI YA CHEYAMANI: Sitifunika Kufooka—Maka-maka Lomba! (Chivumbulutso 12:12)
9:15 YOSIILANA: Pitilizani Kulalikila “Mwakhama”
Ulaliki Wamwayi (Machitidwe 5:42; Mlaliki 11:6)
Kunyumba ndi Nyumba (Machitidwe 20:20)
Ulaliki Wapoyela (Machitidwe 17:17)
Kupanga Ophunzila (Aroma 1:14-16; 1 Akorinto 3:6)
10:05 Nyimbo 153 na Zilengezo
10:15 SEŴELO LA MAU CABE: Yehova Amapulumutsa Anthu Ake (Ekisodo 3:1-22; 4:1-9; 5:1-9; 6:1-8; 7:1-6; 14:5-10, 13-31; 15:1-21)
10:45 Yehova—Citsanzo Cabwino Kwambili ca Kupilila (Aroma 9:22, 23; 15:13; Yakobo 1:2-4)
11:15 Nyimbo 35 na Kupumula
KUMASANA
12:25 Nyimbo za Pavidiyo
12:35 Nyimbo 135
12:40 YOSIILANA: Pililanibe Pamene . . .
Akukucitilani Zopanda Cilungamo (Mateyu 5:38, 39)
Mukukalamba (Yesaya 46:4; Yuda 20, 21)
Muli na Zofooka (Aroma 7:21-25)
Mwapezeka m’Zocitika Zocititsa Manyazi (Agalatiya 2:11-14; Aheberi 12:5, 6, 10, 11)
Mwadwala kwa Nthawi Yaitali (Salimo 41:3)
Munataikilidwa Munthu Amene Mumakonda (Salimo 34:18)
Muzunzidwa (Chivumbulutso 1:9)
13:55 Nyimbo 85 na Zilengezo
14:05 SEŴELO: “Kumbukilani Mkazi wa Loti”—Mbali 1 (Luka 17:28-33)
14:35 YOSIILANA: Kulitsani Makhalidwe Othandiza Kupilila
Cikhulupililo (Aheberi 11:1)
Khalidwe labwino (Afilipi 4:8, 9)
Cidziŵitso (Miyambo 2:10, 11)
Kudziletsa (Agalatiya 5:22, 23)
15:15 Zimene Mungacite kuti ‘Musalephele Ngakhale Pang’ono’ (2 Petulo 1:5-10; Yesaya 40:31; 2 Akorinto 4:7-9, 16)
15:50 Nyimbo 152 na Pemphelo Lothela