Tsiku Laciŵili
“Kondwelani ndi ciyembekezoco. Pililani cisautso” —AROMA 12:12
KUM’MAŴA
- 8:20 Nyimbo za Pavidiyo 
- 8:30 Nyimbo 68 na Pemphelo 
- 8:40 YOSIILANA: Mmene Yehova ‘Amapatsila Mphamvu Zopilila na Kutonthoza’ . . . - Ofooka ndi Ovutika Maganizo (Aroma 15:4, 5; 1 Atesalonika 5:14; 1 Petulo 5:7-10) 
- Ofunikila Thandizo la Kuthupi (1 Timoteyo 6:18) 
- “Onyozeka ndi Ana Amasiye” (Salimo 82:3) 
- Okalamba (Levitiko 19:32) 
 
- 9:50 Nyimbo 90 na Zilengezo 
- 10:00 YOSIILANA: Mangani Nyumba Imene Idzakhalitsa - ‘Khutilani ndi Zimene Muli Nazo pa Nthawiyo’ (Aheberi 13:5; Salimo 127:1, 2) 
- Tetezani Ana Anu ku “Zinthu Zoipa” (Aroma 16:19; Salimo 127:3) 
- Phunzitsani Ana Anu ‘m’Njila Yowayenelela’ (Miyambo 22:3, 6; Salimo 127:4, 5) 
 
- 10:45 NKHANI YA UBATIZO: ‘Musaope Cocititsa Mantha Ciliconse’! (1 Petulo 3:6, 12, 14) 
- 11:15 Nyimbo 139 na Kupumula 
KUMASANA
- 12:35 Nyimbo za Pavidiyo 
- 12:45 Nyimbo 43 
- 12:50 YOSIILANA: Tengelani Citsanzo ca “Anthu Amene Anapilila” - Yosefe (Genesis 37:23-28; 39:17-20; Yakobo 5:11) 
- Yobu (Yobu 10:12; 30:9, 10) 
- Mwana Wamkazi wa Yefita (Oweruza 11:36-40) 
- Yeremiya (Yeremiya 1:8, 9) 
 
- 13:35 SEŴELO: “Kumbukilani Mkazi wa Loti”—Mbali 2 (Luka 17:28-33) 
- 14:05 Nyimbo 75 na Zilengezo 
- 14:15 YOSIILANA: Zolengedwa Zimatiphunzitsa Kupilila - Ngamila (Yuda 20) 
- Mtengo wa Paini (Akolose 2:6, 7; 1 Petulo 5:9, 10) 
- Gulugufe (2 Akorinto 4:16) 
- Mbalame Yochedwa Arctic Tern (1 Akorinto 13:7) 
- Mbalame Yochedwa Plova (Aheberi 10:39) 
- Mtengo wa Akesha (Aefeso 6:13) 
 
- 15:15 Acicepele—Yehova Amakondwela Mukamapilila! (Miyambo 27:11) 
- 15:50 Nyimbo 89 na Pemphelo Lothela