LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • th phunzilo 20 tsa. 23
  • Mawu Otsiliza Ogwila Mtima

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mawu Otsiliza Ogwila Mtima
  • Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa
  • Nkhani Zofanana
  • Kumveketsa Bwino Cifukwa Coŵelengela Lemba
    Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa
  • Yesetsani Kuwafika pa Mtima Omvela
    Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa
  • Kumveketsa Phindu ya Nkhani
    Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa
  • Kumveketsa Bwino Mfundo Zazikulu
    Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa
Onaninso Zina
Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa
th phunzilo 20 tsa. 23

PHUNZILO 20

Mawu Otsiliza Ogwila Mtima

Lemba losagwila

Mlaliki 12:13, 14

ZOFUNIKILA: M’mawu anu othela, limbikitsani omvela anu kuona ubwino wa zimene aphunzila kuti akazigwilitsile nchito.

MOCITILA:

  • Gwilizanitsani mawu anu otsiliza na mfundo yaikulu ya nkhani yanu. Bwelezaninso mfundo zazikulu, kapena zikambeninso m’mawu ena.

  • Limbikitsani omvela anu. Afotokozeleni zofunika kucita, komanso zifukwa zake zomveka. Kambani mocokela pa mtima, komanso mwa cidalilo.

  • Mawu anu otsiliza azikhala osavuta kumva komanso acidule. Osabweletsaponso mfundo zatsopano. Mwa mawu ocepa cabe, alimbikitseninso kucitapo kanthu.

    Tumalangizo tothandizila

    Musathamange nawo mawu otsiliza, komanso safunika kungozimililika. Mawu othela azimveka kuti mukuphela mphongo.

MU ULALIKI

Potsiliza makambilano anu, bwelezani mfundo zimene mufuna kuti womvela wanu akazikumbukile. Ngati makambilano anu adukizidwa, tsilizanibe na mawu abwino. Ngakhale ngati munthuyo ni wamwano, yankhani mwa njila imene pa ulendo wina idzam’limbikitsa kumvetsela.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani