LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • CA-brpgm19 tsa. 3
  • Pezani Mayankho pa Mafunso Aya:

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Pezani Mayankho pa Mafunso Aya:
  • Pulogilamu ya Msonkhano wa Dela wa 2018-2019—Wa Woimila Nthambi
  • Nkhani Zofanana
  • Pezani Mayankho pa Mafunso Aya
    2021-2022 Pulogilamu ya Msonkhano wa Dela—Wa Woimila Nthambi
  • Pezani Mayankho pa Mafunso Aya
    2023-2024 Pulogilamu ya Msonkhano wa Dela—Wa Woimila Nthambi
  • Pezani Mayankho pa Mafunso Awa
    2024-2025 Pulogilamu ya Msonkhano wa Dela—Wa Woimila Nthambi
  • Pezani Mayankho pa Mafunso Aya:
    2018-2019 Pulogilamu ya Msonkhano wa Dela—Wa Woyang’anila Dela
Onaninso Zina
Pulogilamu ya Msonkhano wa Dela wa 2018-2019—Wa Woimila Nthambi
CA-brpgm19 tsa. 3

Pezani Mayankho pa Mafunso Aya:

  1. Kodi mphamvu na nyonga tingazipeze kuti? (Yos. 1:9; Sal. 68:35)

  2. Cofunika n’ciani kuti tipitilize kumanga cikhulupililo cathu? (Aheb. 11:6)

  3. N’cifukwa ciani tili na cidalilo kuti nchito imene Yehova anatipatsa tidzaikwanitsa? (Hag. 2:4-9)

  4. Kodi Yehova amatilimbitsa bwanji pokumana na mayeselo aakulu? (Sal. 18:6, 30; Akol. 4:10, 11)

  5. N’ciani cingathandize acicepele, komanso okwatilana, kucilikiza ucifumu wa Yehova? (Mat. 22:37, 39)

  6. Kodi tingakhale bwanji ‘olimba m’cikhulupililo’ komanso “amphamvu”? (1 Akor. 16:13; Aroma 15:5; Aheb. 5:11–6:1; 12:16, 17)

© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani